Yakobo 1:20 - Buku Lopatulika20 Pakuti mkwiyo wa munthu suchita chilungamo cha Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pakuti mkwiyo wa munthu suchita chilungamo cha Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Paja munthu wokwiya safikapo pa chilungamo chimene amafuna Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Pakuti mkwiyo wa munthu subweretsa chilungamo chimene amafuna Mulungu. Onani mutuwo |