Tito 3:15 - Buku Lopatulika15 Akukupatsa moni onse akukhala pamodzi ndi ine. Pereka moni kwa otikondawo m'chikhulupiriro. Chisomo chikhale ndi inu nonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Akukupatsa moni onse akukhala pamodzi ndi ine. Pereka moni kwa otikondawo m'chikhulupiriro. Chisomo chikhale ndi inu nonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Onse amene ali nane kuno akuti moni. Uperekeko moni kwa onse amene amatikonda chifukwa cha chikhulupiriro. Mulungu akukomereni mtima nonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Onse amene ali ndi ine akupereka moni. Upereke moni kwa amene amatikonda ife mʼchikhulupiriro. Chisomo chikhale ndi inu nonse. Onani mutuwo |