Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Rute 4:18 - Buku Lopatulika

18 Iyo ndiyo mibadwo ya Perezi; Perezi anabala Hezironi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Iyo ndiyo mibadwo ya Perezi; Perezi anabala Hezironi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Tsono zidzukulu za Perezi ndi izi: Perezi adabereka Hezironi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Izi tsono ndizo zidzukulu za Perezi: Perezi anali abambo a Hezironi.

Onani mutuwo Koperani




Rute 4:18
7 Mawu Ofanana  

Ana a Yuda: Perezi, Hezironi, ndi Karimi, ndi Huri, ndi Sobala.


mwana wa Aminadabu, mwana wa Admini, mwana wa Arini, mwana wa Hezironi, mwana wa Perezi, mwana wa Yuda,


ndi nyumba yako inge nyumba ya Perezi, amene Tamara anambalira Yuda, ndi mbeu imene Yehova adzakupatsa ya namwali uyu.


Ndi akazi anansi ake anamutcha dzina, ndi kuti, Kwa Naomi kwambadwira mwana; namutcha dzina lake Obedi; ndiye atate wa Yese atate wa Davide.


ndi Hezironi anabala Ramu, ndi Ramu anabala Aminadabu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa