Rute 3:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anati, Khala ulipo, mwana wanga, mpaka udziwa umo ukhalire mlandu; pakuti munthuyo sadzauleka mpaka atautha mlanduwo lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anati, Khala ulipo, mwana wanga, mpaka udziwa umo ukhalire mlandu; pakuti munthuyo sadzauleka mpaka atautha mlanduwo lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Apongozi akewo adayankha kuti, “Dikira mwana wanga, tiwone m'mene zikhalire zinthu, chifukwa munthuyo salekera pomwepo, koma azikonza zimenezi lero.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka Naomi anati, “Mwana wanga, dikira mpaka titaona mmene zinthu zikhalire chifukwa munthuyu salekera pomwepo, mpaka zinthuzi zitakonzeka lero.” Onani mutuwo |