Rute 3:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo tsopano, mwana wanga, usaope; ndidzakuchitira zonse unenazi; pakuti onse a pa mudzi wa anthu a mtundu wanga adziwa kuti iwe ndiwe mkazi waulemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo tsopano, mwana wanga, usaope; ndidzakuchitira zonse unenazi; pakuti onse a pa mudzi wa anthu a mtundu wanga adziwa kuti iwe ndiwe mkazi waulemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsopano usadandaule, mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene upemphe, pakuti anzanga am'mudzimu akudziŵa kuti ndiwe mkazi wabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo tsopano mwana wanga usaope. Ine ndidzakuchitira chilichonse udzapemphe popeza anzanga onse amʼmudzi muno akudziwa kuti ndiwe mkazi wa khalidwe labwino. Onani mutuwo |