Rute 2:22 - Buku Lopatulika22 Nati Naomi kwa Rute mpongozi wake, Nchabwino, mwana wanga, kuti uzituluka nao adzakazi ake, ndi kuti asakukomane m'munda wina uliwonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Nati Naomi kwa Rute mpongozi wake, Nchabwino, mwana wanga, kuti uzituluka nao adzakazi ake, ndi kuti asakukomane m'munda wina uliwonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Naomi adauza Rute kuti, “Kuli bwino mwana wanga kuti uzipita ndi adzakazi ake, kuwopa kuti ukapita m'munda wina, angakuvute.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Naomi anati kwa Rute mpongozi wake, “Kuli bwino mwana wanga kuti uzipita ndi adzakazi ake kuopa kuti mʼmunda wa munthu wina angakuvute.” Onani mutuwo |