Rute 2:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Rute Mmowabu anati, Ananenanso nane ndithu, Uwaumirire anyamata anga, mpaka atatha kucheka zanga zonse za m'minda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Rute Mmowabu anati, Ananenanso nane ndithu, Uwaumirire anyamata anga, mpaka atatha kucheka zanga zonse za m'minda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono Rute Mmowabuyo adati, “Kuwonjezera pamenepo, munthuyo anandiwuza kuti, ‘Uzitsata antchito angaŵa mpaka atamaliza munda wanga kukolola.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Choncho Rute Mmowabuyo anati, “Iye anandiwuzanso kuti, ‘Uzitsata antchito angawa mpaka atamaliza kukolola munda wonse.’ ” Onani mutuwo |