Rute 2:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mpongozi wake ananena naye, Unakatola kuti khunkha lero? Ndi ntchito udaigwira kuti? Adalitsike iye amene anakusamalira. Ndipo anamfotokozera mpongozi wake munthu amene anakagwirako ntchito, nati, Dzina lake la munthuyo ndinakagwirako ntchito lero ndiye Bowazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mpongozi wake ananena naye, Unakatola kuti khunkha lero? Ndi ntchito udaigwira kuti? Adalitsike iye amene anakusamalira. Ndipo anamfotokozera mpongozi wake munthu amene anakagwirako ntchito, nati, Dzina lake la munthuyo ndinakagwirako ntchito lero ndiye Bowazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Naomi adamufunsa kuti, “Unakakunkha kuti lero? Unakagwira ntchitoyi m'munda mwa yani? Ngwodala munthu amene anakukomera mtimayo.” Rute adauza mpongozi wake za munthu amene adagwirako ntchito, adati, “Munthuyo dzina lake ndi Bowazi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Apongozi akewo anamufunsa kuti, “Kodi lero unakakunkha kuti? Unakagwira kuti ntchitoyi? Adalitsike munthu amene anakukomera mtimayo.” Ndipo Rute anawuza mpongozi wake za munthu amene ku malo ake anakagwirako ntchito. Iye anati, “Munthuyo dzina lake ndi Bowazi.” Onani mutuwo |