Rute 2:18 - Buku Lopatulika18 nalisenza nalowa kumzinda; ndipo mpongozi wake anaona khunkhalo; Rute natulutsanso nampatsa mkute uja anausiya atakhuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 nalisenza nalowa kumudzi; ndipo mpongozi wake anaona khunkhalo; Rute natulutsanso nampatsa mkute uja anausiya atakhuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adatenga bareleyo kupita naye ku mudzi, nakaonetsa mpongozi wake. Atatero, adatulutsa chakudya chimene chidatsalira atakhuta chija, napatsa mpongozi wakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Anasenza barele uja kupita naye ku mudzi, nakaonetsa apongozi ake. Kenaka anatulutsa chakudya chimene chinatsalira atakhuta chija ndi kupatsa apongozi ake. Onani mutuwo |