Rute 2:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo ataumirira kukatola khunkha, Bowazi analamulira anyamata ake ndi kuti, Atole khunkha ngakhale pakati pa mitolo, musamchititse manyazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo ataumirira kukatola khunkha, Bowazi analamulira anyamata ake ndi kuti, Atole khunkha ngakhale pakati pa mitolo, musamchititse manyazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pamene adanyamuka mkaziyo kuti akakunkhe, Bowazi adaŵalangiza antchito ake aja kuti, “Muzimulola mkaziyu kuti azikunkha ngakhale pakati pa mitolo, osamchititsa manyazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Atanyamuka kuti azikakunkha, Bowazi analangiza anyamata ake kuti, “Ngakhale mayiyu azikunkha pakati pa mitolo musamuletse ndi kumuchititsa manyazi. Onani mutuwo |