Rute 1:22 - Buku Lopatulika22 Momwemo anabwera Naomi ndi Rute Mmowabu mpongozi wake pamodzi naye, amene anabwera kuchokera ku dziko la Mowabu; ndipo anafika ku Betelehemu, pakuyamba anthu kucheka barele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Momwemo anabwera Naomi ndi Rute Mmowabu mpongozi wake pamodzi naye, amene anabwera kuchokera ku dziko la Mowabu; ndipo anafika ku Betelehemu, pakuyamba anthu kucheka barele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Umu ndi m'mene Naomi adabwerera kuchokera ku Mowabu pamodzi ndi Rute mpongozi wake wachimowabu uja. Ndipo adafika ku Betelehemu pa nthaŵi yoyamba kudula barele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Naomi anabwerera kuchoka ku dziko la Mowabu pamodzi ndi Rute mpongozi wake. Ndipo anafika ku Betelehemu nthawi yoyamba kukolola barele. Onani mutuwo |