Rute 1:21 - Buku Lopatulika21 Ndinachoka pano wolemera, nandibwezanso kwathu Yehova wopanda kanthu; munditcheranji Naomi, popeza Yehova wandichitira umboni wakunditsutsa, ndi Wamphamvuyonse wandichitira chowawa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndinachoka pano wolemera, nandibwezanso kwathu Yehova wopanda kanthu; munditcheranji Naomi, popeza Yehova wandichitira umboni wakunditsutsa, ndi Wamphamvuyonse wandichitira chowawa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ndidaapita ndili ndi zinthu zambiri, koma Chauta wandibweza ndili wopanda kanthu. Motero munditchulirenji Naomi pamene Mphambe wandisautsa ndi kundigwetsera mavuto oŵaŵa?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ine ndinapita wolemera, koma Yehova wabwera nane wopanda kanthu. Nanga munditchulirenji Naomi pamene Yehova wandisautsa. Wamphamvuzonse uja wandigwetsera mavuto owawa.” Onani mutuwo |