Rute 1:19 - Buku Lopatulika19 Namuka iwo awiriwo mpaka anafika ku Betelehemu. Ndipo kunali pakufika iwo ku Betelehemu, mudzi wonse unapokosera za iwo; nati, Kodi uyu ndi Naomi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Namuka iwo awiriwo mpaka anafika ku Betelehemu. Ndipo kunali pakufika iwo ku Betelehemu, mudzi wonse unapokosera za iwo; nati, Kodi uyu ndi Naomi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Choncho aŵiriwo adapitirira ulendo wao, mpaka adakafika ku Betelehemu. Akaziwo atafika ku Betelehemuko, anthu onse am'mudzimo adatekeseka chifukwa cha iwowo. Tsono akazi ena ankati, “Kodi ameneyu ndi Naomi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Choncho amayi awiriwo anapitiriza ulendo wawo mpaka anakafika ku Betelehemu. Pamene ankafika mu Betelehemu, anthu onse a mʼmudzimo anatekeseka chifukwa cha iwowo ndipo amayi ambiri ankanena kuti, “Kodi uyu nʼkukhala Naomi?” Onani mutuwo |