Rute 1:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo pakuona kuti analimbika kumuka naye, analeka kulankhula naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo pakuona kuti analimbika kumuka naye, analeka kulankhula naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Naomi ataona kuti Rute watsimikiza kupita nao, sadanenenso kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Naomi atazindikira kuti Rute watsimikiza kupita naye, analeka kumukakamiza. Onani mutuwo |