Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Oweruza 9:3 - Buku Lopatulika

3 Pamenepo abale a amake anamnenera mau awa onse m'makutu a eni ake onse a Sekemu; ndi mitima yao inalunjika kutsata Abimeleki; pakuti anati, Ndiye mbale wathu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Pamenepo abale a amake anamnenera mau awa onse m'makutu a eni ake onse a Sekemu; ndi mitima yao inalunjika kutsata Abimeleki; pakuti anati, Ndiye mbale wathu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Achibale a mai wakewo adamlankhulirako kwa anthu onse a ku Sekemu ndipo mitima yao ya anthuwo inali pa Abimeleki pakuti ankati, “Ameneyu ndi mbale wathu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Abale a amayi akewo anamuyankhulira mawu amenewa kwa nzika zonse za ku Sekemu, ndipo mitima ya anthu onse inali pa Abimeleki chifukwa anati, “Uyu ndi mʼbale wathu,”

Onani mutuwo Koperani




Oweruza 9:3
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Labani anati kwa Yakobo, Chifukwa iwe ndiwe mbale wanga, kodi udzanditumikira ine kwachabe? Undiuze ine, malipiro ako adzakhala otani?


Ndipo mthenga unafika kwa Davide nuti, Mitima ya anthu a Israele itsata Abisalomu.


Pakuti woipa adzitamira chifuniro cha moyo wake, adalitsa wosirira, koma anyoza Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa