Oweruza 8:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo ananenanso kwa amuna a ku Penuwele ndi kuti, Ndikabwerera ndi mtendere ndidzagumula nsanja iyi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo ananenanso kwa amuna a ku Penuwele ndi kuti, Ndikabwerera ndi mtendere ndidzagumula nsanja iyi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Apo Gideoni adauza anthu a ku Penuwele kuti, “Pamene ndizikabwerera nditagonjetsa, ndidzagwetsa nsanja ili apayi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Gideoni anawawuzanso kuti, “Ndikamadzabwerera nditawagonjetsa, ndidzagwetsa nsanja iyi.” Onani mutuwo |