Oweruza 8:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Gideoni anati, Chifukwa chake, Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m'dzanja langa, ndidzapuntha nyama yanu ndi minga ya m'chipululu ndi mitungwi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Gideoni anati, Chifukwa chake, Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m'dzanja langa, ndidzapuntha nyama yanu ndi minga ya m'chipululu ndi mitungwi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Gideoni adayankha kuti, “Ai, chabwino! Chauta akapereka Zeba ndi Zalimuna m'manja mwanga, ndidzakukwapulani ndi matsatsa a minga yam'chipululu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Gideoni anayankha kuti, “Mwatero! Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna mʼdzanja langa, ndidzakukwapulani ndi matsatsa a minga ya mʼchipululu.” Onani mutuwo |