Oweruza 8:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Zeba ndi Zalimuna anathawa; koma anawatsata, nagwira mafumu awiri a Midiyani Zeba ndi Zalimuna, nanjenjemeretsa khamu lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Zeba ndi Zalimuna anathawa; koma anawatsata, nagwira mafumu awiri a Midiyani Zeba ndi Zalimuna, nanjenjemeretsa khamu lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Zeba ndi Zalimuna adathaŵa. Gideoni adaŵapirikitsa nagwira mafumu aŵiri a Midiyaniwo, ndipo ankhondo ao onse adathaŵa ndi mantha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Zeba ndi Zalimuna, mafumu awiri a Amidiyani anathawa koma Gideoni anawathamangitsa mpaka kuwagwira. Koma ankhondo awo onse anathawa ndi mantha. Onani mutuwo |