Oweruza 7:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Yehova anati kwa Gideoni, Ndi anthu mazana atatu akukhatira ndidzakupulumutsani, ndi kupereka Amidiyani m'dzanja lako; koma amuke anthu awa onse, yense kumalo kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Yehova anati kwa Gideoni, Ndi anthu mazana atatu akukhatira ndidzakupulumutsani, ndi kupereka Amidiyani m'dzanja lako; koma amuke anthu awa onse, yense kumalo kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndipo Chauta adauza Gideoni kuti, “Ndidzakupulumutsani ndi anthu 300 okhaŵa amene adakhathira pakumwa madzi, ndipo ndidzapereka Amidiyani m'manja mwako. Koma ena onsewo apite kwao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yehova anati kwa Gideoni, “Ndi anthu 300 amene anamwa madzi mokhathira ndi manja awo ndidzakupulumutsani ndipo ndidzapereka Amidiyani mʼmanja mwanu. Koma anthu ena onse apite ku nyumba kwawo.” Onani mutuwo |