Oweruza 7:6 - Buku Lopatulika6 Ndi kuwerenga kwa iwo akukhatira, ndi kuika dzanja lao kukamwa kwao, ndiko mazana atatu; koma ena onse anagwada pakumwa madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndi kuwerenga kwa iwo akukhatira, ndi kuika dzanja lao kukamwa kwao, ndiko mazana atatu; koma ena onse anagwada pakumwa madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono chiŵerengero cha anthu amene adakhathira madzi pakumwa ndi manja chinali anthu 300. Koma anthu ena onse otsala adagwada pansi kuti amwe madzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo anthu 300 anamwa mokhathira, pamene ena onse anagwada pansi pakumwa. Onani mutuwo |