Oweruza 7:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo tsopano, kalalike m'makutu a anthu, ndi kuti, Aliyense wochita mantha, nanjenjemera, abwerere nachoke paphiri la Giliyadi. Ndipo anabwererako anthu zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, natsalako zikwi khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo tsopano, kalalike m'makutu a anthu, ndi kuti, Aliyense wochita mantha, nanjenjemera, abwerere nachoke pa phiri la Giliyadi. Ndipo anabwererako anthu zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, natsalako zikwi khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono ulengeze kwa anthu kuti, ‘Aliyense amene akuchita mantha ndi kunjenjemera, abwerere kwao.’ ” Ndiye anthu okwanira 22,000 adabwerera, natsala 10,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono lengeza kwa anthu kuti, ‘Aliyense amene akuchita mantha ndi kunjenjemera abwerere kwawo, ndipo achoke kuno ku phiri la Giliyadi.’ ” Choncho anthu 22,000 anachoka, ndipo anatsalira anthu 10,000. Onani mutuwo |