Oweruza 7:18 - Buku Lopatulika18 Pamene ndiomba lipenga, ine ndi onse okhala nane, inunso muziomba lipenga pozungulira ponse pa misasa, ndi kunena kuti, Yehova ndi Gideoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pamene ndiomba lipenga, ine ndi onse okhala nane, inunso muziomba lipenga pozungulira ponse pa misasa, ndi kunena kuti, Yehova ndi Gideoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndikaimba lipenga, ineyo pamodzi ndi onse amene ali ndi ine, inunso muimbe malipenga ku mbali zonse za zithando zonse, ndipo mufuule kuti, ‘Lupanga la Chauta ndi la Gideoni.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndikadzaliza lipenga ndi onse amene ali ndi ine, inunso mukalize malipenga kumbali zonse za misasa yonse ndi kufuwula kuti, ‘Lupanga la Yehova ndi la Gideoni.’ ” Onani mutuwo |