Oweruza 5:9 - Buku Lopatulika9 Mtima wanga uvomerezana nao olamulira a mu Israele, amene anadzipereka mwaufulu mwa anthu. Lemekezani Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mtima wanga uvomerezana nao olamulira a m'Israele, amene anadzipereka mwaufulu mwa anthu. Lemekezani Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mtima wanga uli ndi atsogoleri a ankhondo a ku Israele, uli ndi anthu amene adadzipereka mwaufulu, kudzipereka mwaufulu pakati pa anzao. Tamandani Chauta! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mtima wanga uli ndi atsogoleri a Israeli, uli ndi anthu amene anadzipereka okha mwaufulu pakati pa anthu. Tamandani Yehova! Onani mutuwo |