Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Oweruza 4:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo Baraki anati kwa iye, Ukamuka nane, ndidzamuka; ukapanda kumuka nane, sindimuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo Baraki anati kwa iye, Ukamuka nane, ndidzamuka; ukapanda kumuka nane, sindimuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Baraki adayankha kuti, “Mukapita, nanenso ndipita, koma mukapanda kupita, inenso sindipita.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Baraki anamuyankha kuti, “Mukapita nane limodzi ine ndipita. Koma ngati sitipitira limodzi, inenso sindipita.”

Onani mutuwo Koperani




Oweruza 4:8
4 Mawu Ofanana  

Ndipo ndidzamkoka Sisera, kazembe wa nkhondo ya Yabini, akudzere ku mtsinje wa Kisoni, ndi magaleta ake, ndi aunyinji ake; ndipo ndidzampereka m'dzanja lako.


Nati iye, Kumuka ndidzamuka nawe, koma ulendo umukawo, sudzachita nao ulemu; pakuti Yehova adzagulitsa Sisera m'dzanja la mkazi. Motero Debora anauka namuka ndi Baraki ku Kedesi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa