Oweruza 3:4 - Buku Lopatulika4 Amenewo anakhala choyesera Israele kuti Yehova adziwe ngati adzamvere malamulo ake, amene analamulira makolo ao mwa dzanja la Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Amenewo anakhala choyesera Israele kuti Yehova adziwe ngati adzamvere malamulo ake, amene analamulira makolo ao mwa dzanja la Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Adaŵasiya kuti aziyesa nawo Aisraele, kuti aone ngati Aisraele adzamvera malamulo amene Chauta adaapatsa makolo ao kudzera mwa Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwowa Yehova anawasiya kuti aziyesa nawo Aisraeli kuti aone ngati angamvere malamulo a Yehova, amene anapatsa makolo awo kudzera mwa Mose. Onani mutuwo |