Oweruza 2:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova anafa wa zaka zake zana ndi khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova anafa wa zaka zake zana ndi khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Yoswa, mwana wa Nuni, mtumiki wa Chauta, adamwalira ali ndi zaka 110. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova, anamwalira ali ndi zaka 110. Onani mutuwo |