Oweruza 16:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo akalonga a Afilisti anakwera nazo kwa mkaziyo nsinga zatsopano zisanu ndi ziwiri zosauma; ndipo iye anammanga nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo akalonga a Afilisti anakwera nazo kwa mkaziyo nsinga zatsopano zisanu ndi ziwiri zosauma; ndipo iye anammanga nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono akalonga a Afilisti aja adadzampatsa mkaziyo nsinga zisanu ndi ziŵiri zatsopano zosauma, ndipo iye adamangira mwamuna wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsono atsogoleri a Afilisti aja anapita kwa mkazi uja namupatsa zingwe zisanu ndi ziwiri zatsopano zosawuma, ndipo mkaziyo anamanga nazo Samsoni. Onani mutuwo |