Oweruza 15:4 - Buku Lopatulika4 Namuka Samisoni, nagwira ankhandwe mazana atatu, natenga miuni, nalunza michira, naika muuni pakati pa michira iwiri iliyonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Namuka Samisoni, nagwira ankhandwe mazana atatu, natenga miuni, nalunza michira, naika muuni pakati pa michira iwiri iliyonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Motero Samisoni adakagwira nkhandwe mazana atatu nazimangirira michira ziŵiriziŵiri. Kenaka pa mfundo iliyonse ya michirayo adamangirirapo nsakali naziyatsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Choncho Samsoni anapita nakagwira nkhandwe 300 nazimangirira michira ziwiriziwiri ndipo pa fundo iliyonse ya michirayo anamangirira nsakali. Onani mutuwo |