Oweruza 15:2 - Buku Lopatulika2 Nati atate wake, Ndinanenetsa kuti umuda konse, potero ndinampereka kwa bwenzi lako; mng'ono wake sakoma koposa iye nanga? Ukhale naye, m'malo mwa winayu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nati atate wake, Ndinanenetsa kuti umuda konse, potero ndinampereka kwa bwenzi lako; mng'ono wake sakoma koposa iye nanga? Ukhale naye, m'malo mwa winayu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Bamboyo adamuuza kuti, “Ine ndidaatsimikiza kuti mukudana naye kwambiri mkaziyu. Choncho ndidamkwatitsa kwa mnzanu uja. Kodi mng'ono wake si wokongola kupambana iyeyu? Pepani ndithu, ingotengani ameneyu m'malo mwake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Abambo a mkaziyo anati, “Ine ndimaganiza kuti umamuda kwambiri nʼchifukwa chake ndinamupereka kwa mnzako. Kodi mngʼono wake uja sindiye wokongola kupambana iye? Ingotengani ameneyo mʼmalo mwake.” Onani mutuwo |