Oweruza 13:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo panali munthu wina wa Zora wa banja la Adani, dzina lake ndiye Manowa; ndi mkazi wake analibe mwana, sanabale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo panali munthu wina wa Zora wa banja la Adani, dzina lake ndiye Manowa; ndi mkazi wake analibe mwana, sanabala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ku Zora kunali munthu wina, wa fuko la Dani, dzina lake Manowa. Mkazi wake analibe ana, anali wosabereka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ku Zora kunali munthu wina dzina lake Manowa, wochokera ku fuko la Dani. Mkazi wake analibe ana popeza anali wosabereka. Onani mutuwo |