Oweruza 13:11 - Buku Lopatulika11 Nanyamuka Manowa natsata mkazi wake, namdzera mwamuna uja, nanena naye, Kodi ndinu mwamuna uja munalankhula ndi mkaziyu? Ndipo anati, Ndine amene. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Nanyamuka Manowa natsata mkazi wake, namdzera mwamuna uja, nanena naye, Kodi ndinu mwamuna uja munalankhula ndi mkaziyu? Ndipo anati, Ndine amene. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Apo Manowa adanyamuka natsata mkazi wake, ndipo adakafika kumene kunali munthuyo nakamufunsa kuti, “Kodi inu ndinu amene mudaalankhula ndi amaiŵa?” Iye adayankha kuti, “Inde ndinedi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Choncho Manowa ananyamuka namutsatira mkazi wake. Atafika kwa munthuyo anamufunsa kuti, “Kodi ndinu munayankhula ndi mkazi wanga?” Iye anayankha kuti, “Ndine.” Onani mutuwo |