Oweruza 13:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mkaziyo anafulumira nathamanga, nauza mwamuna wake, nanena naye, Taona, wandionekera munthu anandidzerayo tsiku lija. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mkaziyo anafulumira nathamanga, nauza mwamuna wake, nanena naye, Taona, wandionekera munthu anandidzerayo tsiku lija. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mkazi uja adathamanga nakauza mwamuna wake kuti, “Munthu uja adaabwera kuno tsiku lijaliyu wandiwonekeranso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tsono mkaziyo anathamanga kukawuza mwamuna wake kuti, “Wandionekeranso munthu uja amene anabwera kwa ine tsiku lija.” Onani mutuwo |