Oweruza 12:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Yefita anaweruza Israele zaka zisanu ndi chimodzi; nafa Yefita Mgiliyadi, naikidwa m'mzinda wina wa Giliyadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Yefita anaweruza Israele zaka zisanu ndi chimodzi; nafa Yefita Mgiliyadi, naikidwa m'mudzi wina wa Giliyadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yefita adaweruza Aisraele zaka zisanu ndi chimodzi. Pambuyo pake Yefita, amene anali Mgiliyadi, adamwalira, ndipo adaikidwa mu mzinda wake wa Giliyadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yefita anatsogolera Israeli zaka zisanu ndi chimodzi. Kenaka Yefita wa ku Giliyadi anamwalira, ndipo anayikidwa mu mzinda wake ku Giliyadi. Onani mutuwo |