Oweruza 12:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yefita anati kwa iwo, Ine ndi anthu anga tinatsutsana kwakukulu ndi ana a Amoni, koma pamene ndinakuitanani inu simunandipulumutse m'dzanja lao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yefita anati kwa iwo, Ine ndi anthu anga tinatsutsana kwakukulu ndi ana a Amoni, koma pamene ndinakuitanani inu simunandipulumutsa m'dzanja lao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yefita adaŵauza kuti, “Ine ndi anthu anga tidaakangana kwambiri ndi Aamoni. Ndidakuitanani, koma inu simudadzandipulumutse kwa iwowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yefita anayankha kuti, “Ine ndi anthu anga tinakangana kwambiri ndi Aamoni. Ndinakuyitanani koma inu simunandipulumutse mʼmanja mwawo. Onani mutuwo |