Oweruza 11:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yefita anati kwa akulu a Giliyadi, Mukandifikitsanso kwathu kuchita nkhondo ndi ana a Amoni, nakawapereka Yehova pamaso panga, ndidzakhala mkulu wanu kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yefita anati kwa akulu a Giliyadi, Mukandifikitsanso kwathu kuchita nkhondo ndi ana a Amoni, nakawapereka Yehova pamaso panga, ndidzakhala mkulu wanu kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yefita adaŵauza akuluakulu a ku Giliyadiwo kuti, “Mukandibwezeranso kwathu kuti ndikamenye nkhondo ndi Aamoni, ndipo Chauta akandithandiza kuŵagonjetsa, ndidzakhaladi wokulamulirani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yefita anawayankha akuluakulu a ku Giliyadi kuti, “Ngati mundibwezeranso kwathu kuti ndikachite nkhondo ndi Aamoni ndipo Yehova nʼkukandithandiza kuwagonjetsa, ndidzakhaladi wokulamulirani?” Onani mutuwo |