Oweruza 11:6 - Buku Lopatulika6 nati kwa Yefita, Tiye ukhale kazembe wathu kuti tilimbane ndi ana a Amoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 nati kwa Yefita, Tiye ukhale kazembe wathu kuti tilimbane ndi ana a Amoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Akuluakuluwo adauza Yefita kuti, “Bwera udzakhale mtsogoleri wathu kuti timenyane nawo nkhondo Aamoni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwo anati kwa iye, “Bwera ukhale mkulu wathu wankhondo kuti timenyane ndi Amoni.” Onani mutuwo |