Oweruza 10:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anaweruza Israele zaka makumi awiri ndi zitatu, nafa, naikidwa mu Samiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anaweruza Israele zaka makumi awiri ndi zitatu, nafa, naikidwa m'Samiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adaweruza Aisraele zaka 23. Pambuyo pake adamwalira, naikidwa ku Samiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anatsogolera Aisraeli kwa zaka 23, ndipo anamwalira ndi kuyikidwa ku Samiri. Onani mutuwo |