Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Oweruza 1:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo atatero ana a Yuda anatsika kuthirana nao nkhondo Akanani akukhala kumapiri, ndi kumwera ndi kuchidikha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo atatero ana a Yuda anatsika kuthirana nao nkhondo Akanani akukhala kumapiri, ndi kumwera ndi kuchidikha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Kenaka Ayudawo adapita kukamenyana ndi Akanani amene ankakhala m'dziko lamapiri, m'dziko la Negebu lakumwera, ndiponso m'zigwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Kenaka Ayuda anapita kukamenyana ndi Akanaani omwe amakhala ku dziko la ku mapiri, dziko la Negevi kummwera ndiponso mu zigwa.

Onani mutuwo Koperani




Oweruza 1:9
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Abramu anayenda ulendo wake, nayendayenda kunka kumwera.


Ndipo Yoswa ndi Aisraele onse naye anakwera kuchokera ku Egiloni mpaka ku Hebroni, nauthira nkhondo;


Ndipo Yoswa anadza nthawi yomweyo, napasula Aanaki kuwachotsa kumapiri, ku Hebroni, ku Debiri, ku Anabu, ndi ku mapiri onse a Yuda, ndi ku mapiri onse a Israele; Yoswa anawaononga konse, ndi mizinda yao yomwe.


kumapiri ndi kuchigwa, ndi kuchidikha, ndi kumatsikiro, ndi kuchipululu, ndi kumwera: Ahiti, Aamori, ndi Akanani, Aperizi, Ahivi ndi Ayebusi:


Ndipo Yuda anamuka kwa Akanani akukhala mu Hebroni; koma kale dzina la Hebroni ndilo mudzi wa Ariba; ndipo anakantha Sesai, ndi Ahimani, ndi Talimai.


Ndipo ana a Yuda anachita nkhondo pa Yerusalemu, naulanda, naukantha ndi lupanga lakuthwa, natentha mzinda ndi moto.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa