Oweruza 1:6 - Buku Lopatulika6 Koma Adoni-Bezeki anathawa; ndipo anampirikitsa, namgwira, namdula zala zazikulu za m'manja ndi za m'mapazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma Adoni-Bezeki anathawa; ndipo anampirikitsa, namgwira, namdula zala zazikulu za m'manja ndi za m'mapazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adonibezekiyo adathaŵa, koma adamthamangira namgwira, ndipo adadula zala zake zazikulu zakumanja ndiponso zala zake zazikulu zakumwendo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Adoni-Bezekiyo anathawa, koma anamuthamangira ndi kumupeza, namugwira. Atamugwira anamudula zala zake zazikulu za ku manja ndi miyendo. Onani mutuwo |
Pamenepo uiphe nkhosa yamphongoyo, nutapeko pa mwazi wake, ndi kuupaka pa ndewerere ya khutu lamanja la Aroni, ndi pa ndewerere ya khutu lamanja ana ake aamuna, ndi pa chala chachikulu cha dzanja lao lamanja, ndi pa chala chachikulu cha phazi lao lamanja ndi kuuwaza mwaziwo paguwa la nsembe posungulira.