Oweruza 1:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yehova anati, Akwere Yuda; taonani, ndapereka dzikoli m'dzanja lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yehova anati, Akwere Yuda; taonani, ndapereka dzikoli m'dzanja lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chauta adayankha kuti, “Fuko la Yuda ndilo limene lipite. Ndikuŵapatsa dzikolo m'manja mwao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yehova anayankha kuti, “Fuko la Yuda ndilo liyambe kupita. Ndawapatsa dzikolo mʼmanja mwawo.” Onani mutuwo |