Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 35:26 - Buku Lopatulika

26 Koma wakupha munthu akatuluka nthawi iliyonse kulumpha malire a mzinda wake wopulumukirako kumene anathawirako;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Koma wakupha munthu akatuluka nthawi iliyonse kulumpha malire a mudzi wake wopulumukirako kumene anathawirako;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Koma ngati munthu wopha mnzake mwangoziyo atuluka nthaŵi iliyonse kunja kwa malire a mzinda umene adathaŵiramo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 “ ‘Koma ngati wolakwayo atuluka kunja kwa malire a mzinda wopulumukirako kumene anathawira

Onani mutuwo Koperani




Numeri 35:26
3 Mawu Ofanana  

ndipo msonkhano umlanditse wakupha munthu m'dzanja la wolipsa mwazi, ndi msonkhanowo umbwezere kumzinda wake wopulumukirako, kumene adathawirako; ndipo azikhalamo kufikira atafa mkulu wa ansembe wodzozedwa ndi mafuta opatulika.


nakampeza wolipsa mwazi kunja kwa malire a mzinda wake wothawirako, ndipo wolipsa mwazi akapha wakupha munthu, alibe kuchimwira mwazi;


Ndipo kudzakhala kuti aliyense akadzatuluka pa khomo la nyumba yako kubwalo, imfa imeneyi ndi yake, tilibe kupalamula ife; koma aliyense adzakhala ndi iwe m'nyumba, likamfikira dzanja, imfa imeneyi ndi yathu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa