Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 35:24 - Buku Lopatulika

24 pamenepo msonkhano uziweruza pakati pa wokantha mnzakeyo ndi wolipsa mwaziyo monga mwa maweruzo awa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 pamenepo msonkhano uziweruza pakati pa wokantha mnzakeyo ndi wolipsa mwaziyo monga mwa maweruzo awa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 pamenepo mpingo uweruze pakati pa munthu wopha mnzakeyo ndi mbale wa munthu wakufayo, potsata malangizo ameneŵa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 gulu liweruze pakati pa iye ndi wolipsira monga mwa malamulo ake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 35:24
4 Mawu Ofanana  

Ndipo mizindayo ikukhalireni yakupulumuka wolipsa; kuti wakupha mnzake asafe, kufikira ataima pamaso pa msonkhano amweruze.


kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wake, kapena womfunira choipa;


ndipo msonkhano umlanditse wakupha munthu m'dzanja la wolipsa mwazi, ndi msonkhanowo umbwezere kumzinda wake wopulumukirako, kumene adathawirako; ndipo azikhalamo kufikira atafa mkulu wa ansembe wodzozedwa ndi mafuta opatulika.


Ndipo azikhala m'mzindamo mpaka adzaima pamaso pa msonkhano anene mlandu wake, mpaka atafa mkulu wa ansembe wa m'masiku omwewo; pamenepo wakupha mnzake azibwerera ndi kufika kumzinda kwake, ndi nyumba yake, kumzinda kumene adathawako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa