Numeri 35:23 - Buku Lopatulika23 kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wake, kapena womfunira choipa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wake, kapena womfunira choipa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 kapena amulasa ndi mwala woti nkupha munthu, koma amlasa osamuwona mnzakeyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 kapena mosamuona nʼkumuponyera mwala womwe utha kumupha, munthuyo nʼkufa, tsono pakuti sanali mdani wake ndipo sanaganizire zomupweteka, Onani mutuwo |