Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 35:22 - Buku Lopatulika

22 Koma akampyoza modzidzimuka, osamuda, kapena kumponyera kanthu osamlalira,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Koma akampyoza modzidzimuka, osamuda, kapena kumponyera kanthu osamlalira,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 “Koma ngati munthu abaya mnzake mwangozi osati chifukwa cha chidani, kapena alasa mnzake ndi chida osamubisalira,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 “ ‘Koma ngati popanda udani wina uliwonse, mwadzidzidzi akankha wina kapena kumuponyera chinthu osati mwadala,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 35:22
8 Mawu Ofanana  

Koma akapanda kumlalira, koma Mulungu akalola akomane ndi mnzake, ndidzakuikirani pothawirapo iye.


muikire mizinda ikukhalireni mizinda yopulumukirako; kuti wakupha mnzake wosati dala athawireko.


Ndipo akampyoza momkwiyira, kapena kumponyera kanthu momlalira, kuti wafa;


kapena kumpanda ndi dzanja lake momuda, kuti wafa, womkanthayo nayenso amuphe ndithu; ndiye wakupha munthu; wolipsa mwazi aphe wakupha munthuyo akampeza.


kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wake, kapena womfunira choipa;


monga ngati munthu analowa kunkhalango ndi mnzake kutema mitengo, ndi dzanja lake liyendetsa nkhwangwa kutema mtengo, ndi nkhwangwa iguluka m'mpinimo, nikomana ndi mnzake, nafa nayo; athawire ku wina wa mizinda iyi, kuti akhale ndi moyo;


Kuti athawireko wakupha munthu osamupha dala, osadziwa; ndipo idzakhalire inu yopulumukirako, kumpulumuka wolipsa mwazi.


Ndipo akamlondola wolipsa mwazi, asampereke m'dzanja lake wakupha mnzakeyo; pakuti anakantha mnansi wake mosadziwa, osamuda kale.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa