Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 35:18 - Buku Lopatulika

18 Kapena akamkantha m'dzanja muli chipangizo chamtengo, chakufetsa munthu, ndipo wafa, ndiye wakupha munthu; wakupha munthu nayenso amuphe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Kapena akamkantha m'dzanja muli chipangizo chamtengo, chakufetsa munthu, ndipo wafa, ndiye wakupha munthu; wakupha munthu nayenso amuphe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Kapena munthu akamenya mnzake ndi chibonga choti nkupha munthu, mnzakeyo nafadi, ndiye kuti ndi wopha munthu ameneyo. Tsono wopha mnzakeyo ayenera kuphedwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Kapenanso ngati wina ali ndi chibonga mʼdzanja mwake choti nʼkupha nacho munthu, namenya nacho munthu, munthuyo nʼkufa, ndiye kuti iyeyo ndi wakupha, wakuphayo ayenera kuphedwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 35:18
4 Mawu Ofanana  

Zoonatu mwazi wanu wa miyoyo yanu ndidzafuna; padzanja la zinyama zonse ndidzaufuna: ndi padzanja la munthu, padzanja la mbale wake wa munthu ndidzaufuna moyo wa munthu.


Ndipo ndidzaweruza mlandu wako, monga aweruza akazi achigololo ndi okhetsa mwazi; ndipo ndidzakutengera mwazi wa ukali ndi wa nsanje.


Kapena akamkantha m'dzanja muli mwala, wakufetsa munthu, ndipo wafa, ndiye wakupha munthu; wakupha munthu nayenso amuphe ndithu.


Wolipsa mwazi mwini wake aphe wakupha munthuyo; pakumpeza amuphe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa