Numeri 35:14 - Buku Lopatulika14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yordani, ndi mizinda itatu mupereke m'dziko la Kanani, ndiyo yopulumukirako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Mupereke midzi itatu tsidya lino la Yordani, ndi midzi itatu mupereke m'dziko la Kanani, ndiyo yopulumukirako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Mudzapereke mizinda itatu patsidya la kuvuma la mtsinje wa Yordani, ndi mizinda itatu m'dziko la Kanani, kuti ikhale mizinda yothaŵirako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mupereke itatu mbali ino ya Yorodani ndi itatu ina mu Kanaani kuti ikhale mizinda yopulumukirako. Onani mutuwo |