Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 35:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo mizindayo muipereke ikukhalireni mizinda isanu ndi umodzi yopulumukirako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo midziyo muipereke ikukhalireni midzi isanu ndi umodzi yopulumukirako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Mizinda imene mudzaperekeyo idzakhala mizinda isanu ndi umodzi yothaŵirako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Midzi isanu ndi umodzi imene muyiperekeyi idzakhala mizinda yopulumukirako.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 35:13
5 Mawu Ofanana  

Ndi kwa ana a Aroni anapereka mizinda yopulumukirako: Hebroni, ndi Libina ndi mabusa ake, ndi Yatiri, ndi Esitemowa ndi mabusa ake.


Ndipo mizindayo ikukhalireni yakupulumuka wolipsa; kuti wakupha mnzake asafe, kufikira ataima pamaso pa msonkhano amweruze.


Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yordani, ndi mizinda itatu mupereke m'dziko la Kanani, ndiyo yopulumukirako.


Ndipo midziyo muipereke kwa Alevi ndiyo mizinda ija isanu ndi umodzi yopulumukirako; imene muipereke kuti wakupha mnzake athawireko; ndipo pamodzi ndi iyi muperekenso midzi makumi anai ndi iwiri.


Iyi ndi mizinda yoikidwira ana onse a Israele, ndi mlendo wakukhala pakati pao kuti athawireko aliyense wakupha munthu, ndi kuti asafe ndi dzanja la wolipsa mwazi, asanaime pamaso pa msonkhano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa