Numeri 33:56 - Buku Lopatulika56 Ndipo kudzakhala kuti monga ndinayesa kuchitira iwowa, ndidzakuchitirani inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201456 Ndipo kudzakhala kuti monga ndinayesa kuchitira iwowa, ndidzakuchitirani inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa56 Tsono ndidzakuchitani inuyo zimene ndinkaganiza kuti ndiŵachite iwowo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero56 Ndipo pamenepo ndidzachitira inu zomwe ndinaganiza kuwachitira iwowo.’ ” Onani mutuwo |