Numeri 33:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo Aroni wansembe anakwera m'phiri la Hori pa mau a Yehova, nafa komweko, atatuluka ana a Israele m'dziko la Ejipito zaka makumi anai, mwezi wachisanu, tsiku loyamba la mwezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo Aroni wansembe anakwera m'phiri la Hori pa mau a Yehova, nafa komweko, atatuluka ana a Israele m'dziko la Ejipito zaka makumi anai, mwezi wachisanu, tsiku loyamba la mwezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Chauta atamlamula, wansembe Aroni adakwera phiri la Hori nakafera komweko, chaka cha 40 Aisraele atatuluka m'dziko la Ejipito, pa tsiku loyamba la mwezi wachisanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Molamulidwa ndi Yehova, wansembe Aaroni anakwera ku phiri la Hori kumene anakamwalirira pa tsiku loyamba la mwezi wachisanu, mʼchaka cha makumi anayi, Aisraeli atatuluka mʼdziko la Igupto. Onani mutuwo |