Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 31:49 - Buku Lopatulika

49 nati kwa Mose, Atumiki anu anawerenga ankhondo tinali nao, ndipo sanasowe munthu mmodzi wa ife.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 nati kwa Mose, Atumiki anu anawerenga ankhondo tinali nao, ndipo sanasowe munthu mmodzi wa ife.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 Adauza Moseyo kuti, “Atumiki anufe taŵerenga ankhondo amene tikuŵalamulira, ndipo palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene akusoŵa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 iwo anati kwa iye, “Ife anthu anu tawerenga ankhondo amene timawalamulira. Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene wasowa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:49
6 Mawu Ofanana  

Adzaombola moyo wao ku chinyengo ndi chiwawa; ndipo mwazi wao udzakhala wa mtengo pamaso pake.


Pamene uwerenga ana a Israele, monga mwa mawerengedwe ao, munthu yense apereke kwa Yehova chiombolo cha pa moyo wake, pa kuwerengedwa iwowa; kuti pasakhale mliri pakati pao, pakuwerengedwa iwowa.


Pamenepo akazembe a pa ankhondo zikwi, atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, anayandikiza kwa Mose;


Ndipo tabwera nacho chopereka cha Yehova, yense chimene anachipeza, zokometsera zagolide, unyolo, zikwinjiri, mphete zosindikizira, nsapule, ndi mkanda, kuchita chotetezera moyo wathu pamaso pa Yehova.


kuti akwaniridwe mau amene ati, Mwa iwo amene mwandipatsa Ine, sindinataye mmodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa